2 Mafumu 18:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ukuti koma ndiwo mau a pakamwa pokha, Pali uphungu ndi mphamvu ya kunkhondo. Tsono ukhulupirira yani, kuti undipandukira?

2 Mafumu 18

2 Mafumu 18:13-30