2 Mafumu 18:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nthawi yomweyi Hezekiya anakanganula golidi wa pa zitseko za Kacisi wa Yehova, ndi pa zimphuthu adazikuta Hezekiya mfumu ya Yuda, nampereka kwa mfumu ya Asuri.

2 Mafumu 18

2 Mafumu 18:6-20