2 Mafumu 17:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndiwo amene Yehova adapangana nao, nawalamulira, ndi kuti, Musamaopa milungu yina, kapena kuigwadira, kapena kuitumikira, kapena kuiphera nsembe;

2 Mafumu 17

2 Mafumu 17:28-41