2 Mafumu 17:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

mpaka Yehova adacotsa Israyeli pamaso pace, monga adanena mwa dzanja la atumiki ace onse aneneriwo. Momwemo Israyeli anacotsedwa m'dziko lao kumka nao ku Asuri mpaka lero lino.

2 Mafumu 17

2 Mafumu 17:15-28