2 Mafumu 17:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anakaniza mbumba yonse ya Israyeli, nawazunza, nawapereka m'dzanja la ofunkha, mpaka anawataya pamaso pace.

2 Mafumu 17

2 Mafumu 17:19-26