2 Mafumu 17:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace Yehova anakwiya naye Israyeli kwakukuru, nawacotsa pamaso pace osatsala mmodzi, koma pfuko la Yudalokha.

2 Mafumu 17

2 Mafumu 17:8-25