2 Mafumu 16:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ahazi anali wa zaka makumi awiri polowa ufumu wace, nakhala mfumu zaka khumi mphambu zisanu ndi cimodzi m'Yerusalemu; koma sanacita zoongoka pamaso pa Yehova Mulungu wace, ngati Davide kholo lace;

2 Mafumu 16

2 Mafumu 16:1-7