2 Mafumu 16:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu Ahazi anadula matsekerezo a maphaka, nacotsa mbiya pamwamba pao, natsitsa thawale pamwamba pa ng'ombe zamkuwa ziri pansi pace, naziika pa ciunda camiyala.

2 Mafumu 16

2 Mafumu 16:11-20