2 Mafumu 15:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Caka ca makumi atatu mphambu zisanu ndi zitatu ca Azariya mfumu ya Yuda, Zekariya mwana wa Yerobiamu anakhala mfumu ya Israyeli m'Samariya miyezi isanu ndi umodzi.

2 Mafumu 15

2 Mafumu 15:1-16