2 Mafumu 15:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anadwaza mfumu, nakhala iye wakhate mpaka tsiku la imfa yace, nakhala m'nyumba ya padera. Ndipo Yotamu mwana wa mfumu anayang'anira banja la mfumu, naweruza anthu a m'dziko.

2 Mafumu 15

2 Mafumu 15:4-15