2 Mafumu 15:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Masiku awa Yehova anayamba kutumizira Yuda Rezini mfumu ya Aramu, ndi Peka mwana wa Remaliya, amenyane naye.

2 Mafumu 15

2 Mafumu 15:27-38