2 Mafumu 15:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Hoseya mwana wa Ela anamcitira ciwembu Peka mwana wa Remaliya, namkantha, namupha, nakhala mfumu m'malo mwace caka ca makumi awiri ca Yotamu mwana wa Uziya.

2 Mafumu 15

2 Mafumu 15:21-35