2 Mafumu 15:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Caka ca makumi asanu mphambu ziwiri ca Azariya mfumu ya Yuda, Peka mwana wa Remaliya analowa ufumu wace wa Israyeli m'Samariya, nakhala mfumu zaka makumi awiri.

2 Mafumu 15

2 Mafumu 15:23-32