2 Mafumu 15:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Caka ca makumi asanu a Azariya mfumu ya Yuda, Pekahiya mwana wa Menahemu analowa ufumu wace wa Israyeli m'Samariya, nakhala mfumu zaka ziwiri.

2 Mafumu 15

2 Mafumu 15:21-25