2 Mafumu 15:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anali wa zaka khumi ndi zisanu ndi cimodzi polowa ufumu wace, nakhala mfumu zaka makumi asanu mphambu ziwiri m'Yerusalemu; ndi dzina la mace ndiye Yekoliya wa ku Yerusalemu.

2 Mafumu 15

2 Mafumu 15:1-7