2 Mafumu 14:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Natumiza Yoasi mfumu ya Israyeli kwa Amaziya mfumu ya Yuda, ndi kuti, Mtungwi wa ku Lebano unatumiza mau kwa mkungudza wa ku Lebano, ndi kuti, Mpatse mwana wanga wamwamuna mwana wako wamkazi akhale mkazi wace; ndipo Inapitapo nyama ya kuthengo ya ku Lebano, nipondereza mtungwiwo.

2 Mafumu 14

2 Mafumu 14:4-13