2 Mafumu 14:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Caka cakhumi ndi zisanu ca Amaziya mwana wa Yoasi mfumu ya Yuda, Yerobiamu mwana wa Yoasi mfumu ya Israyeli analowa ufumu wace m'Samariya, nakhala mfumu zaka makumi anai mphambu cimodzi.

2 Mafumu 14

2 Mafumu 14:14-29