2 Mafumu 14:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu onse a Yuda anatenga Azariya, (ndiye Uziya), ndiye wa zaka khumi mphambu zisanu ndi cimodzi, namlonga ufumu m'malo mwa atate wace Amaziya,

2 Mafumu 14

2 Mafumu 14:15-23