2 Mafumu 14:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoasi mfumu ya Israyeli anagwira Amaziya mfumu ya Yuda, mwana wa Yoasi mwana wa Ahaziya, ku Betisemesi, nadza ku Yerusalemu, nagamula linga la Yerusalemu kuyambira cipata ca Efraimu kufikira cipata ca kungondya, mikono mazana anai.

2 Mafumu 14

2 Mafumu 14:5-23