2 Mafumu 13:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi Yoasi mwana wa Yoahazi analandanso m'dzanja la Benihadadi mwana wa Hazaeli midzi ija adailanda m'dzanja la Yoahazi atate wace ndi nkhondo. Yoasi anamkantha katatu, naibweza midzi ya Israyeli.

2 Mafumu 13

2 Mafumu 13:19-25