2 Mafumu 13:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Elisa anamwalira, ndipo anamuika. Ndipo magulu a Amoabu analowa m'dziko poyambira caka.

2 Mafumu 13

2 Mafumu 13:14-21