2 Mafumu 13:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nacita coipa pamaso pa Yehova, natsata zolakwa za Yerobiamu mwana wa Nebati, zimene analakwitsa nazo Israyeli; sanazileka.

2 Mafumu 13

2 Mafumu 13:1-3