2 Mafumu 13:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati iye, Tengani mibvi; naitenga, Nati kwa mfumu ya Israyeli, Kwapula pansi; nakwapula katatu, naleka.

2 Mafumu 13

2 Mafumu 13:14-25