2 Mafumu 13:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Elisa anadwala nthenda ija adafa nayo, namtsikira Yoasi mfumu ya Israyeli, namlirira, nati, Atate wanga, atate wanga, gareta wa Israyeli ndi apakavalo ace!

2 Mafumu 13

2 Mafumu 13:5-19