2 Mafumu 13:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Macitidwe ena tsono a Yoasi, ndi zonse anazicita, ndi mphamvu yace yocita nkhondo nayo pa Amaziya mfumu ya Yuda, sizilembedwa kodi m'buku la macitidwe a mafumu a Israyeli?

2 Mafumu 13

2 Mafumu 13:3-13