2 Mafumu 13:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Caka ca makumi atatu ndi zisanu ndi ziwiri ca Yoasi mfumu ya Yuda, Yoasi mwana wa Yoahazi analowa ufumu wace wa Israyeli m'Samariya, nakhala mfumu zaka khumi ndi zisanu ndi cimodzi.

2 Mafumu 13

2 Mafumu 13:6-17