2 Mafumu 12:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo mfumu Yoasi anaitana Yehoyada wansembe, ndi ansembe ena, nanena nao, Mulekeranji kukonza mogamuka nyumba? Tsono musalandiranso ndarama kwa anzanu odziwana nao, kuziperekera mogamuka nyumba.

2 Mafumu 12

2 Mafumu 12:5-11