2 Mafumu 12:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Napereka ndarama zoyesedwa m'manja mwa iwo akucita nchitoyi, akuyang'anira nyumba ya Yehova; ndipo iwo analipira nazo amisiri a mitengo ndi omanga, akugwira nchito ya pa nyumba ya Yehova,

2 Mafumu 12

2 Mafumu 12:1-14