2 Mafumu 12:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Caka cacisanu ndi ciwiri ca Yehu, Yoasi analowa ufumu wace; nakhala mfumu m'Yerusalemu zaka makumi anai; ndi dzina la mai wace ndiye Zibiya wa ku Beereseba.

2 Mafumu 12

2 Mafumu 12:1-9