2 Mafumu 11:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma caka cacisanu ndi ciwiri Yehoyada anaitanitsa atsogoleri a mazana a opha anthu, ndi a otumikira, nabwera nao kwa iye ku nyumba ya Yehova, napangana nao, nawalumbiritsa m'nyumba ya Yehova, nawaonetsa mwana wa mfumu.

2 Mafumu 11

2 Mafumu 11:1-14