2 Mafumu 11:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Namuka anthu onse a m'dzikomo ku nyumba ya Baala, naigumula; maguwa ace a nsembe ndi mafano ace anawaswaiswa, napha Matana wansembe wa Baala ku maguwa a nsembe. Ndipo wansembeyo anaika oyang'anira nyumba ya Yehova.

2 Mafumu 11

2 Mafumu 11:17-21