2 Mafumu 10:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, powafika kalatayo, anatenga ana a mfumu, nawapha amuna makumi asanu ndi awiri, naika mitu yao m'mitanga, naitumiza kwa iye ku Yezreeli.

2 Mafumu 10

2 Mafumu 10:1-11