2 Mafumu 10:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuyambira ku Yordano kum'mawa, dziko lonse la Gileadi, la Agadi, ndi la Arubeni, ndi Amanase, kuyambira ku Aroeri, ndiwo kumtsinje Arinoni, ndilo Gileadi ndi Basana.

2 Mafumu 10

2 Mafumu 10:27-36