2 Mafumu 10:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nalowa Yehu ndi Yehonadabu mwana wa Rekabu m'nyumba ya Baala, nati kwa otumikira Baala, Mufunefune, nimuone asakhale nanu muno otumikira Yehova, koma otumikira Baala okha.

2 Mafumu 10

2 Mafumu 10:15-33