2 Mafumu 10:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehu anatumiza kwa Aisrayeti onse, nadza otumikira Baala onse, wosatsala ndi mmodzi yense wosafika. Nalowa m'nyumba ya Baala; ndi nyumba ya Baala inadzala pha.

2 Mafumu 10

2 Mafumu 10:18-26