2 Mafumu 1:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, watsika mota wakumwamba, nunyeketsa atsogoleri awiri oyamba aja pamodzi ndi makumi asanu ao; koma tsopano moyo wanga ukhale wa mtengo wace pamaso panu.

2 Mafumu 1

2 Mafumu 1:12-18