2 Atesalonika 3:17-18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

17. Cilankhulo ndi dzanja langa Paulo; ndico cizindikilo m'kalata ali yense; ndiko kulemba kwanga.

18. Cisomo ca Ambuye wathu Yesu Kristu cikhale ndi inu nonse.

2 Atesalonika 3