2 Atesalonika 3:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Cotsalira, abale, mutipempherere, kuti mau a Ambuye athamange, nalemekezedwe, monganso kwanu;

2. ndi kuti tilanditsidwe m'manja a anthu osayenerandi oipa; pakuti si onse ali naco cikhulupiriro.

2 Atesalonika 3