2 Atesalonika 2:15-17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

15. Cifukwa cace tsono, abale, cirimikani, gwiritsani miyambo imene tinakuphunzitsani, kapena mwa mau, kapena mwa kalata wathu.

16. Ndipo Ambuye wathu Yesu Kristu, ndi Mulungu Atate wathu amene anatikonda natipatsa elsangalatso cosatha ndi ciyembekezo cokoma mwa cisomo,

17. asangalatse mitima yanu, nakhazikitse inu mu nchito yonse ndi mau onse abwino.

2 Atesalonika 2