2 Akorinto 9:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti kapena akandiperekeze a ku Makedoniya nadzakupezani inu osakonzeka, ife (kuti tisanene inu) tingacititsidwe manyazi m'kulimbika kumene.

2 Akorinto 9

2 Akorinto 9:1-13