2 Akorinto 9:14-15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

14. ndipo iwo, ndi pempherero lao la kwa inu, akhumbitsa inu, cifukwa ca cisomo coposa ca Mulungu pa inu,

15. Ayamikike Mulungu cifukwa ca mphatso yace yace yosatheka kuneneka.

2 Akorinto 9