Ndipo iye wopatsa mbeu kwa wofesa, ndi mkate ukhale cakudya, adzapatsa ndi kucurukitsa mbeu yanu yofesa, nadzaonjezapo pa zipatso za cilungamo canu;