Ndipo tinatumiza mbale wathu awaperekeze iwo, amene tamtsimikizirakawiri kawiri ali wakhama m'zinthu zambiri, koma tsopano wa khama loposatu ndi kulimbika kwakukuru kumene ali nako kwa inu,