2 Akorinto 7:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndilimbika mtima kwambiri pakunena nanu, kudzitamandira kwanga cifukwa ca inu nkwakukuru; ndidzazidwa naco citonthozo, ndisefukira naco cimwemwe m'cisautso cathu conse.

2 Akorinto 7

2 Akorinto 7:1-6