2 Akorinto 7:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ngati ndadzitamandira nako kanthu kwa iye cifukwa ca inu, sindinamvetsedwa manyazi; koma monga tinalankhula zonse ndi inu m'coonadi, koteronso kudzitamandira kwathu kumene kwa Tito, kunakhala coonadi.

2 Akorinto 7

2 Akorinto 7:9-16