2 Akorinto 6:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Musakhale omangidwa m'goli ndi osakhulupira osiyana; pakuti cilungamo cigawanabwanji ndi cosalungama? Kapena kuunika kuyanjana bwanji nw mdima?

2 Akorinto 6

2 Akorinto 6:12-15