2 Akorinto 5:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakutinso ife okhala mu msasawu tibuula, pothodwa; si kunena kuti tifuna kubvulidwa, koma kubvekedwa, kuti caimfaco cimezedwe ndi moyo.

2 Akorinto 5

2 Akorinto 5:1-11