2 Akorinto 5:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kotero kuti ife sitidziwanso munthu tsopano monga mwa thupi; ndipo ngati tazindikira Kristu monga mwa thupi, koma tsopano sitimzindikiranso motero.

2 Akorinto 5

2 Akorinto 5:8-18