2 Akorinto 4:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma takaniza zobisfka za manyazi, osayendayenda mocenjerera, kapena kucita nao mau a Mulungu konyenga; koma ndi maonekedwe a coonadi tidzibvomeretsa tokha ku cikumbu mtima ca anthu onse pamaso pa Mulungu.

2 Akorinto 4

2 Akorinto 4:1-7