2 Akorinto 4:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ife amene tiri ndi moyo tiperekeka kuimfa nthawi zonse, cifukwa ca Yesu, kuti moyonso wa Yesu uoneke m'thupi lathu lakufa.

2 Akorinto 4

2 Akorinto 4:8-17